Zochitika Mu Africa

Mu programu ya Zochitika mu Africa timaulutsa nkhani za ndale, za chuma , za umoyo, za masewera ndi zina zambiri zimene zikuchitika mmaiko amu Africa. Tsamba lathu la Twitter ndi @chinyanja1 pamene tsamba lathu la nkhani pa maikina a internet ndi www.channelafrica.co.za. Mu programu yathu ya lero: Kuwerenga masankho aakulu omwe awaponya mdziko la Mozambique kukupitilira , Lero ndi tsiku lokombukira kufunikila kwa chakudya pa dziko lpansi . Mkonzi wa programu ya lero ndi Madalitso Phiri.