Zochitika mu Africa

Mu programu ya Zochitika mu Africa timaulutsa nkhani za ndale, za chuma , za umoyo, za masewera ndi zina zambiri zimene zikuchitika mmaiko amu Africa. Tsamba lathu la Twitter ndi @chinyanja1 pamene tsamba lathu la nkhani pa maikina a internet ndi www.channelafrica.co.za. Mu programu ya lero muli ndi Zondani Sakala.