Chnyanja News-Zochitika Mu Africa

Mu programu yathu ya lero: 1. Aphungu a Nigeria akupnga malamulo okhudza aphunzitsi amene amanyengerera atsikana apa sukulu kugona nao 2. Anthu wobwera 20,000 anali mu ndende za South Africa kumapeto kwa mwezi wa June caka cino 3. Mapepa woponyera voti ndi katudu wina aperekedwa ku zigao zonse za Mozambique. Ndipo tilinso ndi nkhani zina zambiri. Stella Longwe ndi Madalitso Phiri akubweretserani programuyi.