Subscribe to this channel

You can subscribe to new audio episodes published on this channel. You can follow updates using the channel's RSS feed, or via other audio platforms you may already be using.

RSS Feed

You can use any RSS feed reader to follow updates, even your browser. We recommend using an application dedicated to listening podcasts for the best experience. iOS users can look at Overcast or Castro. Pocket Casts is also very popular and has both iOS and Android versions. Add the above link to the application to follow this podcast channel.

Signup to iono.fm

Sign up for a free iono.fm user account to start building your playlist of podcast channels. You'll be able to build a personalised RSS feed you can follow or listen with our web player.
20
OCT

Malonje

Mu programu ya Malonje omvera amapereka malonje kwa abale ao, abwenzi, omwe amagwira nao ntchito , anthu omwe amawadziwa ndi ena ambiri. Timachezanso ndi akatswiri mu zigao zosiyana: nyimbo, ndale, zachilengedwe, uphunzitsi, ulimi ndi zina zambiri. Mkonzi wa programu ya lero ndi Ziyenela Zimba amene akucheza ndi oimba nyimbo zauzimu Elijah Sakala.
16
OCT

Zochitika Mu Africa

Mu programu ya Zochitika mu Africa timaulutsa nkhani za ndale, za chuma , za umoyo, za masewera ndi zina zambiri zimene zikuchitika mmaiko amu Africa. Tsamba lathu la Twitter ndi @chinyanja1 pamene tsamba lathu la nkhani pa maikina a internet ndi www.channelafrica.co.za. Mu programu yathu ya lero: Kuwerenga masankho aakulu omwe awaponya mdziko la Mozambique kukupitilira , Lero ndi tsiku lokombukira kufunikila kwa chakudya pa dziko lpansi . Mkonzi wa programu ya lero ndi Madalitso Phiri.
15
OCT

Zochitika mu Africa

Mu programu ya Zochitika mu Africa timaulutsa nkhani za ndale, za chuma , za umoyo, za masewera ndi zina zambiri zimene zikuchitika mmaiko amu Africa. Tsamba lathu la Twitter ndi @chinyanja1 pamene tsamba lathu la nkhani pa maikina a internet ndi www.channelafrica.co.za. Mu programu ya lero muli ndi Zondani Sakala.
13
OCT

Malonje

Mu programu ya Malonje omvera amapereka malonje kwa abale ao, abwenzi, omwe amagwira nao ntchito , anthu omwe amawadziwa ndi ena ambiri. Mkonzi komanso muwulutsi wa programu ya lero ndi Blessings Hasitings Jumbe mmzinda wa Blantyre, Malawi.
12
OCT

Malonje

Mu programu ya Malonje omvera amakhala ndi mwai wakupereka malonje kwa abale ao, abwenzi ao, omwe amagwira nao ntchito ndi ena ambiri amene amawadziwa. Mkonzi wa programu ya tsiku la lero ndi Blessings Hastings Jumbe mmzinda wa Blantyre , Malawi.
10
OCT

Chnyanja News-Zochitika Mu Africa

Mu programu yathu ya lero: 1. Aphungu a Nigeria akupnga malamulo okhudza aphunzitsi amene amanyengerera atsikana apa sukulu kugona nao 2. Anthu wobwera 20,000 anali mu ndende za South Africa kumapeto kwa mwezi wa June caka cino 3. Mapepa woponyera voti ndi katudu wina aperekedwa ku zigao zonse za Mozambique. Ndipo tilinso ndi nkhani zina zambiri. Stella Longwe ndi Madalitso Phiri akubweretserani programuyi.

1002 episodes

« Back 1—12 More »