Subscribe to this channel

You can subscribe to new audio episodes published on this channel. You can follow updates using the channel's RSS feed, or via other audio platforms you may already be using.

RSS Feed

You can use any RSS feed reader to follow updates, even your browser. We recommend using an application dedicated to listening podcasts for the best experience. iOS users can look at Overcast or Castro. Pocket Casts is also very popular and has both iOS and Android versions. Add the above link to the application to follow this podcast channel.

Signup to iono.fm

Sign up for a free iono.fm user account to start building your playlist of podcast channels. You'll be able to build a personalised RSS feed you can follow or listen with our web player.
10
MAY

CHIPANI CHOSUTSA CHA UPND MDZIKO LA ZAMBIA CHAPANGA MGWILIZANO NDI ZIPANI ZISANU

Chipani chachikulu chotsutsa boma cha mdziko la Zambia ca UPND chapanga mgwirizano ndi zipani zisanu zazing'ono pansi pa dzina limodzi lakuti The Zambia We Want Alliance. Cholinga cha mgwirizanowu ndikugwetsa chipani cholamula boma ca PF, Patriotic Front, cha President Edgar Chagwa Lungu mmasankho apatatu amene adzachitika pa 12 August chaka chino

ENGLISH: Zambian opposition party the UPND has formed an alliance with five opposition parties ‘The Zambia we want alliance’ with the intention to defeat the Zambian current ruling party the Patriotic front (PF) in the upcoming August 12 August tripartite elections
10
MAY

ANTHU OPOSA 25 THOUSOND AKHALA OPANDA MAGETSI KUMPOTO KWA MOZAMBIQUE

Anthu oposa 25 thousand akhala opanda magetsi kwa miyezi ingapo mchigawo cha ku mpoto mdziko la Mozambique chifukwa cha ziwembu zomwe zikupitilira mchigawochi.
ENGLISH: More than 25,000 people in northern Mozambique are going to be without electricity for the foreseeable future as power infrastructure had been vandalised by the Islamist militants in recent attacks
10
MAY

MALAWI: MABUNGWE ALANKHULA PA CHIGAMULO CHOTI AKULU AWILI A MEC ALEMBEDWENSO

limodzi mwa mabungwe omenyela ufulu mdziko la Malawi lathilira ndemanga pa chigamulo cha khothi kuti akulu akulu awili a bungwe loyendetsa masankho la MEC omwe anachotsedwa ntchito abwelere mmaudindo omwe anali nawo mmbungweli.

ENGLISH : A civil society organisation in Malawi CDEDI has commented on the court’s ruling that the two Malawi electoral commissioners who were removed from their positions be reinstated.
10
MAY

KUSINTHA KWA NYENGO MDZIKO LA ZAMBIA

Boma la Zambia likulimbikitsa anthu kudzala mitengo pofuna kuchepetsa kusintha kwa nyengo komwe kukupangitsa kuti mvula isamagwe bwino.

ENGLISH: Due to climate change in Zambia that has changed rainfall patterns; the government is encouraging citizens to plant trees .
07
MAY

ALIMI AKUKUMANA NDI MAVUTO OSIYANA KU MOZAMBIQUE

Alimi ku Mozambique akukumana ndi mavuto osiyana siyana ngakhale akulandila thandizo la ndalama kuchokela ku boma.

ENGLISH: Farmers in Mozambique are facing a lot of challenges despite getting financial assistance from government.
07
MAY

MABUNGWE KU MALAWI APEMPHA MAKHOTHI KUTI AZIWUNIKA MILANDU YOZEMBETSA ANA

Mabungwe oyima pawokha mdziko la Malawi apempha ma khothi kuti aziwunika milandu yokhudza kuzembetsa ana mwansanga chifukwa choti milandu yambiri ikumakhala osaweluzidwa.

ENGLISH: Civil society organizations in Malawi have asked Malawian courts to speed up child trafficking cases as most cases remain unresolved for so many years.
07
MAY

NDONDOMEKO YOFUNA KUPELEKA KATEMELA WACHIWIRI KU MALAWI

Boma la Malawi lati katemela wa covid 19 wachiwiri adzapelekedwa mwezi wa mmawa wa June mmalo mwa mwezi uno ndi cholinga choti katemela wambiri azakhale atafika mmadela onse a mdzikolo.

ENGLISH: Malawi will roll out second dose of covid 19 vaccines in June as opposed to May 2021 with the aim to have enough vaccine available in all regions.
07
MAY

MAMEMBALA AMBILI A ZIPANI KU ZAMBIA AYAMBA KULOWA MCHIPANI CHOLAMULA CHA PF

Mamembala ambiri a mzipani zosutsa mdziko la Zambia ayamba kuchoka mzipani zawo ndi kulowa mchipani cholamula cha PF pokhulupilira kuti chipanichi chidzapambana masankho pa 21 august chaka chino. Mabungwe ndi akatswili ena a ndale akhumudwa ndi mchitidwewu.

ENGLISH: Most opposition members from various political parties in Zambia are moving to the ruling party the PF hoping that the party will win the August 12, 2021 tripartite elections.
07
MAY

ZAMBIA WAYIKA MALAMULO OTHANDIZA MZIKA ZA DZIKOLI ZA KUNJA KUTENGA ZITUPA

Boma la Zambia lakhazikitsa malamulo othandiza mzika za dzikoli zomwe zili kunja potenga zitupa. Zambia zaka zammbuyo anavomeleza anthu a mdzikolo kukhala ndi umzika uwiri wina wa mdzikoli ndi wina wa komwe amakhala.
ENGLISH: Zambian government has introduced new regulations for citizens in the diaspora to acquire passports in the country.
07
MAY

20% YA ANTHU MMAYIKO 15 A MU AFRICA INAKANA KATEMELA WA COVID 19

Kafukufuku wa bungwe lowona za matenda osiyana ndi kapewedwe la Africa Centres for Disease Control and Prevention amene anapangidwa mmaiko 15 amu Africa wapeza kuti anthu pa gao la 20 % mmaikowa anakana kubayidwa katemela wa Covid-19.
ENGLISH: Africa Center for Diseases Control and Prevention (ACDC) research from 15 African countries states that 20% of the population have refused to take Covid-19 vaccine.
07
MAY

MALAWI AYAMBA KUDALIRA NTCHITO ZA MIGODI

Dziko la Malawi tsopano liyamba kudalira ntchito za migodi pa chuma chake mmalo mwa Fodya. Chaposachedwa president wa dzikolo Lazarus Chakwela anatsimikiza kuti nthawi yafika kuti Malawi achilimike pa ntchito za migodi
ENGLISH: The Malawian Government will start relying on mining industries in its economy, moving away from tobacco which has been the country’s source of revenue for decades.
06
MAY

GOLD MARKETS - MALAWI

Bank yayikulu ya Reserve mdziko la Malawi itsegula msika wa golide mwezi uno ndipo ndi koyamba mumbili ya dzikoli.

ENGLISH : The Malawian Government is introducing gold market through the Reserve Bank for the first time in the country’s history.

1302 episodes

« Back 1—12 More »